Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 7
  • May 22-28

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 22-28
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 7

May 22-28

2 MBIRI 25-27

  • Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambiri Kuposa Pamenepa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 26:4, 5​—Kodi chitsanzo cha Uziya chikutiphunzitsa chiyani zokhudza kufunika kokhala ndi munthu wolimba mwauzimu woti azitilangiza? (w07 12/15 10 ¶1-2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 25:1-13 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 15)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 10 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 3)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 136

  • Moyo Wosatha ndi Wabwino Kwambiri Kuposa Zinthu Zimene Tingasiye (Mko 10:29, 30): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi lonjezo la Yesu lopezeka pa Maliko 10:29, 30, likutilimbikitsa kuchita chiyani? Kodi Yesu anachita chiyani pamene abale ake sanamukhulupirire poyamba? Kodi tiyenera kumakumbukira chiyani zokhudza achibale athu omwe si a Mboni?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 46

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 51 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena