Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 14
  • June 26–July 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 26–July 2
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 14

June 26–July 2

EZARA 1-3

  • Nyimbo Na. 75 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Eza 1:5, 6​—Kodi tingaphunzire chiyani kuchokera kwa Aisiraeli ena amene anatsala ku Babulo? (w06 1/15 19 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Eza 2:58-70 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 9)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 10 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 58

  • “Mumasangalala Mukamayambitsa Nkhani”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 49 mfundo 1-5

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena