Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 4
  • May 8-14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 8-14
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 4

May 8-14

2 MBIRI 20-21

  • Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 21:14, 15​—Kodi ulosi wa Eliya wokhudza Yehoramu unakwaniritsidwa bwanji? (it-1 1271 ¶1-2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 20:20-30 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Baibulo​—Chv 21:3, 4. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 9)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 119

  • “Kodi Mwakonzeka Kukumana ndi Mavuto Azachuma?”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Ikambidwe ndi mkulu. Tchulaninso zilengezo zochokera ku ofesi ya nthambi kapena ku bungwe la akulu ngati zilipo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 45 mfundo 1-3

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Yatsopano ya Msonkhano wa 2023 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena