Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 10
  • June 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 5-11
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 10

June 5-11

2 MBIRI 30-31

  • Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kusonkhana Pamodzi Kumatithandiza”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 30:20​—Kodi tingaphunzirepo chiyani kuchokera pa zimene Yehova anachita pomvetsera Hezekiya? (w18.09 6 ¶14-15)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 31:11-21 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 20)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01. (th phunziro 18)

  • Nkhani: (5 min.) w19.01 11-12 ¶13-18​—Mutu: Tizitamanda Yehova Poyankha Pamisonkhano. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 74

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Uzikonzekera Zimene Ukayankhe: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana mafunso awa: Kodi mungakonzekere bwanji zoti mukayankhe pamisonkhano? N’chifukwa chiyani tiyenera kukhalabe osangalala ngakhale pamene sanatipatse mwayi woyankha?

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff kubwereza gawo 3

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena