Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 January tsamba 10
  • February 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 5-11
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 January tsamba 10

FEBRUARY 5-11

SALIMO 1-4

Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Khalani ku Mbali ya Ufumu wa Mulungu

(10 min.)

[Onerani VIDIYO ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Masalimo.]

Maboma a anthu adzipanga kukhala adani a Mulungu (Sl 2:2; w21.09 15 ¶8)

Yehova akupereka mwayi kwa anthu onse kuti asankhe kukhala ku mbali ya Ufumu wake (Sl 2:10-12)

Zithunzi: 1. Anthu okwiya anyamula zikwangwani ndipo akuchita zionetsero. 2. Mnyamata wanyamula mbendera ndipo akuchemerera masewera. 3. Mwana wa sukulu akuimba nyimbo ya fuko. 4. Msilikali wanyamula mfuti. 5. Anthu awiri amene akuimira pa zisankho ali pa mtsutso. 6. Mzimayi akuponya voti.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndine wotsimikiza mtima kusatenga nawo mbali pa zochitika za ndale za m’dzikoli, ngakhale zitaoneka kuti kuchita zimenezi kukhoza kundibweretsera mavuto?’—w16.04 29 ¶11.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 1:4—Kodi anthu oipa amafanana bwanji ndi “mankhusu amene amauluzika ndi mphepo”? (it-1 425)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 3:1–4:8 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kukambirana Mwachibadwa—Zomwe Filipo Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani lmd phunziro 2 mfundo 1-2.

5. Kukambirana Mwachibadwa—Zomwe Mungachite Potsanzira Filipo

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 2 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 32

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 5 ¶9-15, bokosi patsamba 41

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 61 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena