APRIL 22-28
MASALIMO 32-33
Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. N’chifukwa Chiyani Muyenera Kuulula Tchimo Lalikulu?
(10 min.)
Davide ankavutika mumtima mwake pamene ankabisa tchimo lake, mwina lomwe anachita ndi Batiseba (Sl 32:3, 4; w93 3/15 9 ¶7)
Davide anaulula tchimolo kwa Yehova ndipo anamukhululukira (Sl 32:5; cl 262 ¶8)
Davide anamva bwino Yehova atam’khululukira (Sl 32:1; w01 6/1 29 ¶7)
Tikachita tchimo lalikulu tiyenera kuvomereza modzichepetsa n’kuulula zomwe tachitazo kwa Yehova ndiponso kumupempha kuti atikhululukire. Tiyeneranso kupempha thandizo kwa akulu, omwe angatithandize kukhalanso pa ubwenzi wabwino ndi Yehova. (Yak 5:14-16) Tikachita zimenezi Yehova amatitsitsimula.—Mac 3:19.
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 33:6—Kodi “mpweya” wa m’kamwa mwa Yehova n’chiyani? (w06 5/15 19 ¶13)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 33:1-22 (th phunziro 11)
4. Kudzichepetsa—Zomwe Paulo Anachita
(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 4 mfundo 1-2.
5. Kudzichepetsa—Zomwe Mungachite Potsanzira Paulo
(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 4 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo Na. 74
6. Zofunika Pampingo
(15 min.)
7. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 8 ¶22-24, bokosi patsamba 67