Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 March tsamba 12
  • April 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 15-21
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 March tsamba 12

APRIL 15-21

MASALIMO 29-31

Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Chilango Chimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda

(10 min.)

Yehova anabisa nkhope yake chifukwa choti Davide sanamvere (Sl 30:7; it-1 802 ¶3)

Davide analapa ndipo anapempha Yehova kuti amukomere mtima (Sl 30:8)

Yehova sanapitirizebe kukwiyira Davide (Sl 30:5; w07 3/1 19 ¶1)


N’kutheka kuti Salimo 30 limafotokoza zimene zinachitika Davide atachita tchimo lowerenga Aisiraeli.​—2Sa 24:25.

Bambo wochotsedwa akupemphera m’galimoto yake asanakalowe m’Nyumba ya Ufumu.

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi chilango chochotsa munthu mumpingo chimamuthandiza bwanji kusonyeza kuti walapa?​—w21.10 6 ¶18.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 31:23​—Kodi Yehova amalanga bwanji kwambiri munthu wodzikuza? (w06 5/15 19 ¶12)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 31:1-24 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(1 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Lalikirani mwachidule kwa munthu amene watanganidwa. (lmd phunziro 5 mfundo 3)

5. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Sonyezani mayi vidiyo ya ana ndipo mufotokozereni mmene angapezerenso mavidiyo ena ambiri. (lmd phunziro 3 mfundo 3)

6. Ulendo Wobwereza

(3 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Uzani munthu amene anakanapo kuphunzira Baibulo m’mbuyomu kuti muziphunzira naye. (lmd phunziro 8 mfundo 3)

7. Kuphunzitsa Anthu

(4 min.) lff phunziro 14 mfundo 5 (th phunziro 6)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 45

8. N’chifukwa Chiyani Timakhulupirira . . . Kuti Mulungu Amatikonda?

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO. Kenako funsani omvera funso ili:

Kodi zimene zinachitikira m’baleyu zatiphunzitsa chiyani zokhudza chikondi cha Mulungu?

9. Lipoti la Dipatimenti Yoona za Mapulani ndi Zomangamanga la 2024

(8 min.) Nkhani. Onerani VIDIYO.

10. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 8 ¶13-21

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 99 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena