Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 May tsamba 4
  • May 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 13-19
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 May tsamba 4

MAY 13-19

MASALIMO 38-39

Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Musamangokhalira Kudziimba Mlandu

(10 min.)

Kudziimba mlandu kwambiri kuli ngati kunyamula katundu wolemera kwambiri (Sl 38:3-8; w20.11 27 ¶12-13)

M’malo momangoganizira zimene munalakwitsa m’mbuyomu, muzikhala wofunitsitsa kuchita zomwe zingasangalatse Yehova (Sl 39:4, 5; w02 11/15 20 ¶1-2)

Ngakhale mukuona kuti n’zovuta kupemphera chifukwa choti mukudziimba mlandu, muzipempherabe (Sl 39:12; w21.10 15 ¶4)

Zithunzi: 1. M’bale akuvutika kunyamula katundu yemwe ndi wolemera kwambiri. 2. M’bale yemwe uja watula katundu uja, ndipo akuyang’ana kutsogolo molimba mtima.

Ngati mukudziimba mlandu kwambiri, muzikumbukira kuti Yehova ‘amakhululukira ndi mtima wonse’ anthu ochimwa omwe alapa.​—Yes 55:7.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 39:1​—Kodi ndi pa nthawi iti pamene tingagwiritse ntchito mfundo yakuti “ndidzaphimba pakamwa panga kuti ndisalankhule”? (w22.09 13 ¶16)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 38:1-22 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kulankhula Mwaluso​—Zomwe Paulo Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 5 mfundo 1-2.

5. Kulankhula Mwaluso​—Zomwe Mungachite Potsanzira Paulo

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 5 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 44

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 9 ¶17-24, bokosi patsamba 73

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena