Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 July tsamba 2
  • July 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 1-7
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 July tsamba 2

JULY 1-7

MASALIMO 57-59

Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mfumu Sauli ali pakati pa asilikali ake ndipo akuyang’ana kumwamba uku akulankhula pamene wagwira malaya ake omwe adulidwa m’mphepete.

Mfumu Sauli ndi asilikali ake atalephera kugwira Davide

1. Yehova Amasokoneza Anthu Amene Amatsutsa Atumiki Ake

(10 min.)

Davide anakakamizika kuthawa Mfumu Sauli (1Sa 24:3; Sl 57, kamutu)

Yehova anasokoneza zochita za anthu amene ankatsutsa Davide (1Sa 24:7-10, 17-22; Sl 57:3)

Nthawi zina, zimene anthu otsutsa amafuna kuchita zimalephereka (Sl 57:6; bt 220-221 ¶14-15)

Abale ndi alongo omwe anatumizidwa ku Siberia.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimadalira Yehova ndikamatsutsidwa?’—Sl 57:2.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 57:7—Kodi kutsimikiza mtima kumatanthauza chiyani? (w23.07 18-19 ¶16-17)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 59:1-17 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kuchita Khama—Zomwe Paulo Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 7 mfundo 1-2.

5. Kuchita Khama—Zomwe Mungachite Potsanzira Paulo

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 7 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 65

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 12 ¶1-6, bokosi patsamba 96

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 78 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena