Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 September tsamba 8-9
  • September 30–October 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 30–October 6
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 September tsamba 8-9

SEPTEMBER 30–OCTOBER 6

MASALIMO 90-91

Nyimbo Na. 140 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Muzikhulupirira Yehova Kuti Mukhale ndi Moyo Wautali

(10 min.)

N’zosatheka kuti anthufe patokha titalikitse moyo wathu (Sl 90:10; wp19.3 5 ¶3-5)

Yehova ndi “Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale” (Sl 90:2; wp19.1 5, bokosi)

Akhoza kupereka ndipo adzapereka moyo wosatha kwa anthu amene amamukhulupirira (Sl 21:4; 91:16)

Dokotala akupereka mapepala ndi cholembera kwa m’bale yemwe ali pabedi lakuchipatala usiku.

Musasokoneze ubwenzi wanu ndi Yehova polola thandizo la mankhwala lomwe ndi losemphana ndi mfundo zake.—w22.06 18 ¶16-17.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 91:11—Kodi tiziliona bwanji thandizo limene angelo amapereka? (wp17.5 5)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 91:​1-16 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Popanda kukambirana za Baibulo, chezani ndi munthuyo m’njira yoti mudziwe mmene Baibulo lingamuthandizire pa moyo wake. (lmd phunziro 1 mfundo 3)

5. Ulendo Woyamba

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. (lmd phunziro 1 mfundo 4)

6. Nkhani

(5 min.) lmd zakumapeto A mfundo 5—Mutu: Mungathe Kudzakhala Ndi Moyo Padzikoli Mpaka Kalekale. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 158

7. Muzisangalala Ndi Kuleza Mtima kwa Mulungu—Mmene Yehova Amaonera Nthawi

(5 min.) Nkhani yokambirana.

Onerani VIDIYO. Kenako funsani funso ili:

  • Kodi kuganizira mmene Yehova amaonera nthawi kungatithandize bwanji kuti tiziyembekezera malonjezo ake moleza mtima?

Anthu ali pamwamba pa phiri ndipo akuyang’ana kumwamba komwe kwadzaza nyenyezi.

8. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September

(10 min.) Onerani VIDIYOYI.

9. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 16 ¶1-5, , bokosi patsamba 128

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 68 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena