Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 September tsamba 12
  • October 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 September tsamba 12

OCTOBER 14-20

MASALIMO 96-99

Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Muzilengeza Uthenga Wabwino”

(10 min.)

Muziuza ena uthenga wabwino (Sl 96:2; w11 3/1 6 ¶1-2)

Muziwaphunzitsa za uthenga wabwino wonena za Tsiku la Chiweruzo (Sl 96:​12, 13; w12 9/1 16 ¶1)

Muziwathandiza kudziwa cholinga cha Yehova choti padziko lapansi padzaze anthu amene amatamanda dzina lake (Sl 99:​1-3; w12 9/15 12 ¶18-19)

M’bale wachikulire akucheza ndi bambo wina pampando kupaki.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 96:1—Kodi mawu akuti “nyimbo yatsopano” amanena za chiyani m’malo ambiri amene mawuwa akupezeka? (it-2 994)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 98:1–99:9 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kudzipereka—Zomwe Yesu Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani lmd phunziro 10 mfundo 1-2.

5. Kudzipereka—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 10 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 9

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 16 ¶10-18

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena