Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 September tsamba 13
  • October 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 21-27
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 September tsamba 13

OCTOBER 21-27

MASALIMO 100-102

Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Muziyamikira Chikondi Chokhulupirika cha Yehova

(10 min.)

Muzikonda kwambiri Yehova (Sl 100:5; w23.03 12 ¶18-19)

Muzipewa zinthu zimene zingawononge ubwenzi wanu ndi Yehova (Sl 101:​2, 3; w23.02 17 ¶10)

Muzipewa anthu amene amanena zabodza zokhudza Yehova ndi gulu lake (Sl 101:5; w11 7/15 16 ¶7-8)

M’bale akuyang’ana pafoni yake. Pakuoneka ma positi a pa malo ochezera a pa intaneti, kuphatikizapo podikasiti, nkhani, zithunzi, mameseji, komanso tizizindikiro tosiyanasiyana.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndikhoza kuwononga ubwenzi wanga ndi Yehova chifukwa cha mmene ndimagwiritsira ntchito intaneti?’

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 102:6—N’chifukwa chiyani wolemba salimoli anadziyerekezera ndi mbalame yotchedwa vuwo? (it-2 596)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 102:​1-28 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunziro 2 mfundo 3)

5. Ulendo Wobwereza

(5 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (lmd phunziro 9 mfundo 4)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira

(4 min.) Chitsanzo. ijwbq 129—Mutu: Kodi Baibulo Linasinthidwa Kapena Kusokonezedwa? (th phunziro 8)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 137

7. ‘Ndikumamatirani, Inuyo Mundigwire Mwamphamvu’

(15 min.)

Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO. Kenako funsani mafunso awa:

  • Kodi Anna anasonyeza bwanji chikondi chokhulupirika?

  • Kodi tingamutsanzire bwanji?

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 17 ¶1-7

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 96 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena