Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 November tsamba 9
  • December 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 9-15
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 November tsamba 9

DECEMBER 9-15

SALIMO 119:1-56

Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Kodi Wachinyamata Angakhale Bwanji Woyera pa Moyo Wake?”

(10 min.)

Akamadzifufuza nthawi zonse (Sl 119:9; w87 11/1 18 ¶10)

Akamatsatira zikumbutso za Mulungu (Sl 119:24, 31, 36; w06 6/15 25 ¶1)

Akamapewa kuyang’ana zinthu zopanda pake (Sl 119:37; w10 4/15 20 ¶2)

M’bale wachinyamata akuphunzira Baibulo payekha.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndamva zikumbutso ziti zimene zingandithandize kukhalabe ndi makhalidwe abwino?’

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 119—Kodi Salimoli linalembedwa m’njira yotani, nanga n’kutheka kuti analilemba choncho chifukwa chiyani? (w05 4/15 10 ¶2)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 119:1-32 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Yambani kukambirana ndi munthu amene mwakumana naye mumsewu pamene mukulalikira ulaliki wa kunyumba ndi nyumba. (lmd phunziro 1 mfundo 4)

5. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Pa ulendo wapita, mwininyumbayo anakuuzani kuti wachibale wake kapena mnzake wamwalira. (lmd phunziro 9 mfundo 3)

6. Nkhani

(5 min.) ijwyp 83—Mutu: Kodi Ndingatani Kuti Ndisamagonje Poyesedwa? (th phunziro 20)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 40

7. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December

(10 min.) Onerani VIDIYOYI.

8. Zofunika Pampingo

(5 min.)

9. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 19 ¶6-13

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena