Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 November tsamba 8
  • December 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 November tsamba 8

DECEMBER 2-8

MASALIMO 113-118

Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Kodi Yehova Tidzamubwezera Chiyani?

(10 min.)

Yehova amatiteteza, amachita nafe zinthu mokoma mtima komanso amatipulumutsa (Sl 116:6-8; w01 1/1 11 ¶13)

Tingabwezere Yehova ngati pa moyo wathu timatsatira mfundo zake komanso malamulo ake (Sl 116:12, 14; w09 7/15 29 ¶4-5)

Tingabwezere Yehova popereka “nsembe zoyamikira” (Sl 116:17; w19.11 22-23 ¶9-11)

Banja likuyang’ana kutsogolo molimba mtima. Zithunzi zosonyeza mmene angagwiritsire ntchito nthawi yawo: 1. Akuonera pulogalamu yosayenera pa TV; akuphunzira Baibulo limodzi. 2. Apita kumsika ndipo agula zinthu zambiri; akulalikira pogwiritsa ntchito kashelefu.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 116:15—Kodi anthu a Mulungu “okhulupirika” amene akutchulidwa mu vesili ndi ndani? (w12 5/15 22 ¶1-3)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 116:1–117:2 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kulangiza Molimba Mtima—Zomwe Yesu Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 12 mfundo 1-2.

5. Kulangiza Molimba Mtima—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 12 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 60

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 19 ¶1-5, bokosi patsamba 149-150

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena