Magazini Yophunzira
DECEMBER 2022
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JANUARY 30–FEBRUARY 26, 2023
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Pa nthawi ya Ulamuliro wa Zaka 1,000, m’bale akusangalala kuwonjezera luso lomwe ankafuna kudzakhala nalo (Onani nkhani yophunzira 50, ndime 19)