Nkhani Zimene Zatuluka pa JW Library Komanso JW.ORG
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Laibulale Yokwanira M’dzanja Limodzi
Onani zomwe zimachitika pokonza komanso kuwonjezera zinthu zina pa JW Library®.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Muziona Moyenera Zinthu Zimene Zimakukwiyitsani
M’malo molola kuti zinthu zomwe zimakukwiyitsani zichititse kuti muzikangana, muziziona moyenera.
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
“Misewu Ndi Imene Inali Nyumba Yanga”
Zimene Antonio anakumana nazo m’dzikoli lomwe ndi lodzaza ndi zachiwawa, kugwiritsa ntchito mankhwala osokoneza bongo komanso kuledzera zinamuchititsa kumaona kuti moyo ulibe cholinga. Ndiye n’chiyani chinamuthandiza kusintha maganizo?