Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w23 January tsamba 32
  • Mungaphunzirenso Izi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mungaphunzirenso Izi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Kanani Nkhani Zachabe’
    Nsanja ya Olonda—1994
  • Mungaphunzirenso Izi
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Muzikhulupirira Kwambiri Gulu la Yehova
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
w23 January tsamba 32

Mungaphunzirenso Izi

Kodi mumakonda kuwerenga mbiri ya moyo wa abale ndi alongo athu?

Banja lina lomwe limawerenga nkhani imodzi m’mawa uliwonse linati: “Nkhanizi zimatilimbikitsa komanso kutithandiza kukhala osangalala. Zimatikumbutsa kuti nafenso tingakhale okhulupirika pa chilichonse.” Mlongo winanso yemwe amamva choncho analemba kuti: “Nkhanizi ndi zotonthoza, zolimbikitsa komanso zokhazika mtima pansi. Mbiri ya abale ndi alongo omwe amafotokozedwa imasonyeza kuti moyo wawo ndi watanthauzo. Zimandilimbikitsa kuti ndizichita zambiri mu utumiki komanso kuthandiza ana anga kuti adzachite utumiki wa nthawi zonse.”

Nkhanizi zingakuthandizeni kuti muzichita zambiri potumikira Yehova, musiye makhalidwe oipa komanso muzipirira mosangalala ndiponso mokhulupirika mayesero ovuta. Kodi mungapeze bwanji nkhanizi?

  • Fufuzani pa gawo lakuti “Mbiri za a Mboni za Yehova Ena” pa jw.org kapena pa JW Library®.

  • Fufuzani “Mbiri za a Mboni za Yehova Ena” pa Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI kapena Watchtower Library.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena