Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w23 March tsamba 32
  • Mungaphunzirenso Izi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mungaphunzirenso Izi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Mmene Mungagwiritsire Ntchito Gawo Lakuti “Zatsopano”
  • JW Library
  • JW.ORG
  • Mungapeze Nzeru Zokuthandizani pa JW.ORG
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Zimene Mungapezenso Pawebusaiti
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Mungapeze Thandizo
    Galamukani!—2020
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
w23 March tsamba 32

Mungaphunzirenso Izi

Mmene Mungagwiritsire Ntchito Gawo Lakuti “Zatsopano”

Pagawo lakuti “Zatsopano” pa JW Library komanso pa jw.org pamapezeka zinthu zomwe zangotulutsidwa kumene. Kodi mungagwiritse ntchito bwanji gawoli kuti mudziwe nkhani zimene zangochitika kumene?

JW Library

  • Nkhani iliyonse ikatulutsidwa, imaikidwa pagulu la nkhani zofanana ndi imene yangotuluka kumeneyo. Gulu la nkhanizo likaonekera pagawo lakuti “Zatsopano,” mukhoza kulipanga dawunilodi. Kenako mungawerenge nkhani yatsopano, yomwe imakhala pamwamba pa nkhani zonse. Nkhanizo zimasanjidwa potengera tsiku lomwe zinatuluka.

  • Mwina simungathe kuwerenga zinthu monga magazini pa nthawi imodzi. Pofuna kukuthandizani kudziwa magazini yomwe simunamalize kuwerenga, mungathe kuika magaziniyo pagawo lakuti Favorites, mpaka pamene mudzamalize kuiwerenga.

JW.ORG

Zinthu zina monga nkhani komanso zilengezo zimapezeka pa jw.org pokha osati pa JW Library. Muziona pafupipafupi gawo lakuti “Zatsopano” pawebusaitiyi kuti muone nkhani zatsopano.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena