Zimene Zili M’magaziniyi
M’MAGAZINIYI MULI
Nkhani Yophunzira 40: December 8-14, 2025
6 Yehova Amatithandiza Kuti ‘Tizisangalala Kwambiri’
Nkhani Yophunzira 41: December 15-21, 2025
12 Chikondi cha Mulungu Chidzakhalapo Mpaka Kalekale
Nkhani Yophunzira 42: December 22-28, 2025
18 Mungatani Kuti Mapemphero Anu Azikhala Ochokera Pansi pa Mtima?
Nkhani Yophunzira 43: December 29, 2025–January 4, 2026
24 Muzikumbukira Kupempherera Anthu Ena
30 Abale Awiri Atsopano a M’Bungwe Lolamulira
32 Mfundo Zothandiza Pophunzira—Muzitsatira Ndandanda Yanu Yowerengera Baibulo Tsiku ndi Tsiku