Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yb17 tsamba 82-83
  • Georgia

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Georgia
  • Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017
yb17 tsamba 82-83
Wa Mboni za Yehova akulalikira m’dera lina lamapiri ku Georgia

Georgia

UTHENGA wabwino unafalikira m’dziko la Georgia mosaonekera ngati mmene Yesu ananenera mufanizo la zofufumitsa. (Mat. 13:33) Mofanana ndi zofufumitsa, poyamba zotsatira za ntchito yathu yolalikira m’dzikoli sizinkaoneka bwinobwino. Koma kenako uthenga wabwino unafalikira ndipo unasintha miyoyo ya anthu ambiri.

Werengani nkhani yosangalatsayi ndiponso yolimbikitsa yonena za abale a m’dziko la Georgia. Abalewa anasonyeza chikondi, chikhulupiriro, kumvera, khama komanso kulimba mtima ‘pa nthawi yabwino ndi pa nthawi yovuta.’​—2 Tim. 4:2.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena