LEVITIKO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
3
4
5
Machimo osiyanasiyana komanso nsembe zake (1-6)
Nsembe zimene anthu osauka ankapereka (7-13)
Nsembe yakupalamula imene munthu amapereka chifukwa chakuti wachimwa mosadziwa (14-19)
6
7
Malangizo okhudza nsembe (1-21)
Lamulo loletsa kudya mafuta komanso magazi (22-27)
Gawo la ansembe (28-36)
Mfundo zomaliza zokhudza nsembe (37, 38)
8
9
10
11
12
13
14
15
16
17
Chihema, malo operekera nsembe (1-9)
Analetsa kudya magazi (10-14)
Malamulo okhudza nyama zopezeka zitafa (15, 16)
18
19
20
Kulambira Moleki; zamizimu (1-6)
Mukhale oyera ndipo muzilemekeza makolo (7-9)
Opalamula milandu yokhudza kugonana ayenera kuphedwa (10-21)
Mukhale oyera kuti mupitirize kukhala mʼdziko (22-26)
Anthu ochita zamizimu aziphedwa (27)
21
Ansembe azikhala oyera komanso osadetsedwa (1-9)
Mkulu wa ansembe asamadzidetse (10-15)
Ansembe asamakhale ndi chilema (16-24)
22
23
24
Mafuta a nyale zamuchihema (1-4)
Mitanda ya mkate wachionetsero (5-9)
Munthu wonyoza dzina la Mulungu aziponyedwa miyala (10-23)
25
Chaka cha Sabata (1-7)
Chaka cha Ufulu (8-22)
Kubweza katundu kwa mwiniwake (23-34)
Zoyenera kuchita ndi anthu osauka (35-38)
Malamulo okhudza ukapolo (39-55)
26
Muzipewa kulambira mafano (1, 2)
Madalitso obwera chifukwa cha kumvera (3-13)
Chilango cha munthu wosamvera (14-46)
27
Kuwombola zinthu zimene zinaperekedwa mochita kulonjeza (1-27)
Zinthu zoyenera kuwonongedwa zoperekedwa kwa Yehova (28, 29)
Kuwombola chakhumi (30-34)