RUTE
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Banja la Elimeleki linasamukira ku Mowabu (1, 2)
Naomi, Olipa ndi Rute anakhala amasiye (3-6)
Rute anakhala wokhulupirika kwa Naomi ndi Mulungu wake (7-17)
Naomi anabwerera ku Betelehemu ndi Rute (18-22)
2
Rute anakakunkha mʼmunda wa Boazi (1-3)
Rute anakumana ndi Boazi (4-16)
Rute anauza Naomi kuti Boazi anamukomera mtima (17-23)
3
Naomi anapereka malangizo kwa Rute (1-4)
Rute ndi Boazi kopunthira mbewu (5-15)
Rute anabwerera kwa Naomi (16-18)
4
Boazi anakhala wowombola (1-12)
Boazi ndi Rute anabereka Obedi (13-17)
Mzere wa makolo a Davide (18-22)