Zamkatimu
May 8, 2000
Mabomba Okwirira Pansi—Kodi N’kuthana Nawo Bwanji?
Mabomba okwirira pansi amapha kapena kulemaza anthu pafupifupi 26,000 chaka chilichonse. Ambiri amene amavutika ndi mabombaŵa ndi anthu wamba, ndiponso ana. Kodi kuopsa kwa mabomba okwirira pansi kudzathadi?
4 Kupenda Mavuto Odza ndi Mabomba Okwirira
8 Dziko Lopanda Mabomba Okwirira
10 Nkhani za pa TV—Kodi Ndi Zambiri Motani Zimene Zimakhala Zofunikadi?
11 Mgwirizano wa Ulaya—N’chifukwa Chiyani Ungakhale Wofunika?
13 Kodi Ulaya Adzagwirizanadi?
25 Kodi Mbalame Ingam’phunzitsenji Mkaidi?
12 “Ufa!”
28 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
Kubereka Ana—Kodi N’kumene Kumachititsa Mwamuna Kukhala Weniweni? 13
31 AIDS mu Afirika—Kodi Pali Chiyembekezo Chotani M’zaka Chikwi Zatsopano?
32 Mmene Mungasangalalire ndi Moyo wa Banja
Njira Yogonjetsera Kutaya Mtima 20
Kutaya mtima n’kofala pakati pa anthu onse. Kodi Baibulo lingakuthandizeni motani kuti muthane ndi maganizo otayiratu chiyembekezo chonse?
Loida sanali kulankhula chibadwire. Kodi chinam’thandiza kuyamba kulankhula atatha zaka 18 wosalankhula n’chiyani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Chikuto: Copyright Adrian Brooks Photography
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Copyright David Chancellor/Alpha