Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g00 12/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2000
  • Nkhani Yofanana
  • Kuthana ndi Matenda a Kachiwalo Kotchedwa Prostate
    Galamukani!—2000
  • Ana Ayenera Kufunidwa Ndiponso Kukondedwa
    Galamukani!—2000
  • Zamkatimu
    Galamukani!—2000
  • Zamkatimu
    Galamukani!—2002
Onani Zambiri
Galamukani!—2000
g00 12/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

December 8, 2000

Mavuto a Ana Njira Yodzawathetseratu Yapezeka!

Ana ambiri sakondedwa ndiponso safunidwa. Ana miyandamiyanda ali ndi umphaŵi ndipo amafa adakali aang’ono chaka n’chaka. Kodi zosoŵa zawo zidzakwaniritsidwadi?

3 Kufunafuna Njira Zothetsera Mavuto a Ana Kukupitirizabe

6 Ana Ayenera Kufunidwa Ndiponso Kukondedwa

10 Njira Yodzawathetseratu Yapezeka!

16 Kuthana ndi Matenda a Kachiwalo Kotchedwa Prostate

26 Lingaliro la Baibulo

Kodi Sayansi Ingabweretse Moyo Wosatha?

28 Ngakhale Ndili Wolumala Ndine Wosangalala

32 Zisonyezero za Voliyumu 81 ya Galamukani!

Kodi N’chifukwa Chiyani Abambo Anatichokera? 13

N’chifukwa chiyani abambo ena amanyanyala mabanja awo? Kodi ana awo angathetse bwanji kuwawidwa maganizo?

Kuthana ndi Ziyeso Mwamphamvu ya Mulungu 20

Akristu a ku Ukraine anakumana ndi ziyeso pamene dzikolo linali mbali ya Soviet Union. Ŵerengani kuti mudziŵe zina mwa ziyeso zimenezi ndiponso kuti Akristuwo anathana nazo bwanji.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena