Zamkatimu
June 8, 2002
Kodi Sayansi ndi Chipembedzo Zingagwirizane
Anthu ena amaona kuti sayansi ndi chipembedzo n’zinthu zosagwirizana. Kodi zinthu zimenezi n’kutheka kuzigwirizanitsa?
3 Sayansi ndi Chipembedzo Zikulimbana
4 Kodi Chilengedwe Chonsechi Ndiponso Zamoyozi Zinakhalako Bwanji?
8 Kugwirizanitsa Sayansi ndi Chipembedzo
12 Dzitetezeni Kuti Musagonthe M’kutu!
15 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
Kodi Ndingapeze Bwanji Mnzanga Wabwino Wogona Naye m’Chipinda Chimodzi?
18 Tizilombo Tochotsa Nyansi Mogometsa
19 Kudalirana kwa Mayiko N’kolimbikitsa Komanso N’kokayikitsa
22 Kodi Kudalirana kwa Mayiko Kungathetsedi Mavuto Athu?
27 Kudalirana kwa Mayiko Kumene Kudzakupindulitseni
32 Tikukuitanani ku Msonkhano Wachigawo wa “Olengeza Ufumu Achangu”
Kodi Akristu Ayenera Kulalikira Anthu Ena? 30
Kodi Mulungu ndiponso Yesu amaiona bwanji nkhaniyi?