Zamkatimu
January 8, 2001
Kodi Ukwati Wathu Tingaupulumutse?
Kodi kukhala mu ukwati wopanda chikondi ndiko njira yabwinopo poyerekeza ndi kusudzulana? Kodi mwamuna ndi mkazi amene chikondi chawo chazirala angapulumutse motani ukwati wawo?
3 Zikuvuta Kuchoka mu Ukwati Wopanda Chikondi
4 N’chifukwa Chiyani Chikondi Chimazirala?
7 Kodi Pali Chifukwa Chokhalira ndi Chiyembekezo?
8 Ukwati Wanuwo Utha Kupulumuka!
15 Inali Yoyamba Zaka 100 Zapitazo
21 Kodi N’kuti Kumene Mungapeze Maphunziro Abwino Kwambiri?
22 Ntchito Yamaphunziro Yofala Kwambiri
32 Sakhulupirira Kwenikweni Koma Akufufuzabe
Maphunziro Othandiza kwa Moyo Wonse 28
Ŵerengani za ndawala yophunzitsa imene imagogomezera miyezo yapamwamba yamakhalidwe, yopereka moyo wabwinopo, ndiponso yopereka chiyembekezo cholimba cha m’tsogolo.