Zamkatimu
May 8, 2001
Kodi Akaidi Angatheke Kuwasintha?
Kaŵirikaŵiri, ndende zimangophunzitsa umbanda woopsa kwambiri. Koma taŵerengani mumve mmene akaidi ena awathandizira kusinthiratu.
4 Kodi Njira Yothetsera Vutolo Ndiyo Ikulikulitsanso?
8 Kodi Kusinthadi Ambanda N’kotheka?
3 Dziko la Soviet Union Liukira Chipembedzo
4 Amene Anaukiridwa Kwambiri ndi Soviet Union
9 Mmene Zipembedzo Zinapulumukira
13 Kodi Tsogolo la Chipembedzo N’lotani?
Kusefukira kwa Madzi ku Mozambique—Momwe Akristu Anasamalira Anthu Ovutikawo 24
Ŵerengani mmene chikhulupiriro choona chinakulira mphamvu m’kati mwa masoka.
Kodi Yehova Anali Mulungu wa Fuko la Ayuda? 28
Kodi timadziŵa bwanji kuti Yehova ndi Mulungu wa anthu a mitundu yonse.