Zamkatimu
June 8, 2001
Thanzi Labwino kwa Onse—Kodi Zingatheke?
Bungwe la World Health Organization linakhazikitsa cholinga chabwino chopezera “anthu onse padziko lapansi thanzi labwino.” Kodi sayansi ya zamankhwala idzachitadi zimenezo?
3 Thanzi Labwino kwa Onse—Kodi Zingatheke?
4 Sayansi Yamakono ya Zamankhwala—Kodi Ingafike Pati?
9 Thanzi Labwino kwa Onse—Lifika Posachedwapa!
15 Kulimbana ndi Vuto la Uchigaŵenga
19 Uchigaŵenga Utha Posachedwapa!
24 Ulendo Wokaona Malo ku Ghana
28 Kodi Kupulula Anthu Kungadzachitikenso?
32 Tikulandirani ku Msonkhano Wachigawo wa “Aphunzitsi a Mawu a Mulungu”!
Kodi Nditani Kuti Ubale Wanga ndi Agogo Ulimbe? 21
Phunzirani njira zothandiza zimene mungatsate kuti mulimbitse ndi kusunga ubale wanu ndi agogo.
Kodi Zipembedzo Zonse ndi Misewu Yopita kwa Mulungu? 30
Anthu ambiri angayankhe kuti inde. Kodi Baibulo limati bwanji?