Zamkatimu
November 8, 2001
Kuthandiza Akazi Omenyedwa ndi Amuna Awo
Padziko lonse akazi amamenyedwa ndi amuna awo. Ena amaphedwa. Kodi angadziteteze bwanji?
5 Kodi Amuna Amamenyeranji Akazi?
9 Kuthandiza Akazi Omenyedwa ndi Amuna Awo
11 “Nthaŵi Zina Ndimangoona Ngati N’kutulo Ndithu!”
19 Gwiritsani Ntchito Mankhwala Mwanzeru
22 N’chifukwa Chiyani Anthu Amatopa Nawo Moyo?
32 Kodi Ana Tiyenera Kuwalangiza Bwanji?
Matatu—Galimoto Zochititsa Chidwi za ku Kenya Zonyamula Apaulendo 16
Kwina kulikonse anthu amakhala ndi njira zawo zonyamulira anthu apaulendo. Kodi kuyenda pa matatu n’kosiyana bwanji ndi njira zinazo?