Zamkatimu
January 8, 2002
Kulimba Mtima Panthaŵi ya Zoopsa
Tikusimba nkhani zochepa zosonyeza mmene anthu analimbira mtima, kuchita chifundo, ndiponso kupirira pa September 11, 2001, pamene nyumba zosanja ziŵiri zimene zinali likulu la za malonda padziko lonse lotchedwa World Trade Center zinagwa.
3 Tsiku Limene Nyumba Zosanja Ziŵiri Zinagwa
10 Thandizo Ndiponso Kukoma Mtima kwa Anthu a M’madera Osiyanasiyana
13 Kodi Chakudya Chanu N’chosakayikitsa?
14 Kodi Chakudya Chathu Tikuchitani?
18 Zimene Mungachite Kuti Chakudya Chikhale Chosakayikitsa
21 Munthu Aliyense Adzakhala Nacho Chakudya Chosakayikitsa
23 Kudalira Mulungu Kunandilimbitsa
Kodi Akristu Ayenera Kuchita Nawo Chikondwerero cha Chaka Chatsopano? 28
Kodi chikondwerero cha chaka chatsopano chinayambira kuti? Kodi n’chotsutsana ndi zimene Baibulo limaphunzitsa?
Kodi Pali Vuto Ngati Nditakhala Pachibwenzi Ndidakali Wamng’ono? 30
Kodi kuchita zibwenzi ndi khalidwe labwino? Kapena kumabweretsa mavuto ena amene munthu ayenera kuwaona bwino kuti adziŵedi ngati kuli kwanzeru kutero?
[Mawu a Chithunzi patsamba 3]
CHIKUTO: AP Photo/Matt Moyers;
masamba 2 ndi 3: Steve Ludlum/NYT Pictures