Zamkatimu
July 8, 2002
Kodi Apolisi Timawafuna Chifukwa Chiyani?
Padziko lonse, apolisi amalimbana ndi chintchito choonetsetsa kuti anthu akutsatira malamulo a boma ndiponso kuti akukhala mwabata. Kodi zinthu zikuwayendera bwanji?
3 Kodi Apolisi Ndi Ofunika Chifukwa Chiyani?
5 Kutetezedwa Ndi Apolisi N’kolimbitsa Mtima Komanso N’kokayikitsa
10 Kodi Apolisi Ali ndi Tsogolo Lotani?
16 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
Kodi Mnzanga Amene Ndimagona Naye M’chipinda Chimodzi Ndingagwirizane Naye Bwanji?
19 Ukapolo Ndi Khalidwe Lankhanza Lomwe Lidakalipobe
20 Tinayamba Kalekale Kulimbana Ndi Ukapolo
22 Nthaŵi Imene Ukapolo Udzathe!
27 Ndinali Wandale Tsopano Ndinasanduka Mkristu Wosakhudzidwa N’zandale
32 “Kanafika pa Nthaŵi Yofunika”
Kodi Kutengeka ndi Zithunzi Zolaula Kulibe Vuto Lililonse? 13
Kodi ndi mfundo za m’Baibulo zotani zimene zimagwira ntchito pa nkhani yokhudza zithunzi zolaula? Kodi zithunzi zimenezi zimangowasangalatsa anthu popanda kuwasokoneza m’njira inayake? Kapena kodi zingathedi kum’sokoneza Mkristu kuti asamachite zinthu zoyenera?