Zamkatimu
September 8, 2002
Zinyalala—Kodi Tichita Kukwiririka Nazo?
Anthu akuchita zinthu zochulukitsa zinyalala kuposa kale lonse, ndipo zimenezi zikupangitsa kuti chilengedwe chikhale ndi mavuto osaneneka. Kodi ndi zinthu zotani zimene zachititsa kuti anthu akhale owononga chonchi, ndipo kodi tingalimbane nazo bwanji?
3 Kukhala M’dziko Lokonda Kutaya Zinthu
5 Kodi Pali Njira Yothetsera Vutoli?
9 Kulimbana Ndi Mavuto a M’dziko Lokonda Kutaya Zinthu
15 Kugwiritsa Ntchito Galamukani! Mwanjira Yabwino
19 Manambala—Kodi Mumakhudzidwa Nawo?
20 Anthu Amatengeka Mtima Ndi Manambala
22 Kodi Muyenera Kudalira Manambala Pazochita Zanu?
25 Mfundo Zodalirika Zokhudza Tsogolo Lathu
26 Mapemphero Amene Mulungu Amamva
32 “Ndifunika Kuti Ndidziŵe Bwino Nkhaniyi”
Kodi Ngozi Zapamsewu—Sizingakuchitikireni? 12
Dziŵani mmene mungapeŵere zinthu ziŵiri zazikulu zimene zimachititsa ngozi zoopsa zapamsewu.
Kodi Ndichititse Opaleshoni Kuti Ndikhale Wokongola? 16
Achinyamata ambirimbiri akufuna kuchititsa opaleshoni monga njira yodzikongoletsera. Kodi zimenezi si zoopsa?