Zamkatimu
March 8, 2003
Kusoŵa Zakudya M’thupi“Mliri Wobisika”
N’chifukwa chiyani anthu ambiri—makamaka ana—amasoŵa chakudya? Ŵerengani kuti mudziŵe zimene zimayambitsa matenda a kusoŵa kwa zakudya m’thupi ndi mmene mungawapeŵere.
5 Kodi Pagona Vutoli Mpati, Nanga Kuipa Kwake N’kotani?
11 “Mliri Wobisikawu” Utha Posachedwa!
13 Kusonyezana Chikondi Panthaŵi ya Mavuto
24 Kusiya Ntchito Yopha Anthu N’kuyamba Ntchito Yolimbikitsa Mtendere
28 Kodi Nsapato Zanu Zimakukwanani Bwinobwino?
31 “Galamukani! Inapulumutsa Moyo Wanga!”
Msamuko Waukulu Wochititsa Chidwi 15
Nyumbu mamiliyoni ambiri zikagundika nacho chiulendo kudutsa madambo a m’Africa muno, zimachititsa chidwi ndipo sungaiŵale.
Kodi Ndizionera Matepi a Nyimbo? 19
Matepi ambiri amaonetsa zachiwawa ndi zachiwerewere. Ndiye mudzatani?
[Chithunzi patsamba 2]
Somalia
[Mawu a Chithunzi]
© Betty Press/Panos Pictures
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
CHIKUTO: UN/DPI Photo by Eskinder Debebe