Zamkatimu
May 8, 2004
Kodi Mungatani Mukamavutitsidwa Kuntchito?
Mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kulimbana nalo bwinobwino vutoli mwinanso kulipeŵa kumene.
3 N’kuntchito Kapena N’kunkhondo?
5 Kodi Zimatani Kuti Ayambe Kuwavutitsa
7 Zoyenera Kuchita Kuti Mukhale Pamtendere Kuntchito
11 Chiyembekezo Chimathandizadi?
12 Kodi Timafuniranji Chiyembekezo?
15 Mungathe Kuthetsa Khalidwe Lotaya Mtima
17 Kodi Chiyembekezo Chodalirika Mungachipeze Kuti?
21 Ngati Mwana Wanu Wakhanda Sasiya Kulira
22 Nkhani ya Chiŵerengero cha Anthu, M’Baibulo, ndi M’tsogolo
22 Banja Liyesedwa Chikhulupiriro
N’chifukwa Chiyani Ukwati Tiyenera Kuuona Kuti N’ngopatulika? 28
Ukwati wanu ungayende bwino malingana ndi mmene inuyo mumauonera.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
© Alejandro Balaguer/PromPerú