Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g04 8/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2004
  • Nkhani Yofanana
  • Zamkatimu
    Galamukani!—2003
  • Kuchoka ku Olympia Kukachitira ku Sydney
    Galamukani!—2000
  • Zolinga za Olimpiki Zakanika
    Galamukani!—2000
  • Zamkatimu
    Galamukani!—2005
Onani Zambiri
Galamukani!—2004
g04 8/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

August 8, 2004

Dzitetezeni kwa Anthu Oba Mwachinyengo

Kuchita zinthu zingapo zofunika kungakuthandizeni kwambiri kudziteteza kuti asakubereni mwachinyengo.

3 Kuba Mwachinyengo ndi Vuto Lapadziko Lonse

5 Mmene Mungadzitetezere Kwa Anthu Oba Mwachinyengo

10 Kodi Mfundo za Makhalidwe Abwino Mungazipeze Kuti?

15 Msamariya Wachifundo Wamakono

18 Mphaka Amene Ali Pangozi Kwambiri Padziko Lonse Lapansi

19 Anthu Amabadwa ndi Ludzu Lofuna Kuphunzira

20 Mmene Mungalimbikitsire Ana Kuti Azikonda Kuphunzira

27 Tinalengedwa Kuti Tiziphunzira Mpaka Kalekale

29 Nkhaŵa Imene Munthu Ali Nayo pa Maonekedwe Ake Ikasanduka Matenda

31 Zoseŵeretsa Ana Zabwino Kwambiri

32 ‘Limandithandiza Kupirira Mavuto’

Kodi Pali Cholakwika Kugonana Tisanakwatirane? 12

Achinyamata ambiri amamva kuti ayenera kugonanako ndi munthu wina. Koma kodi maganizo a Akristu ayenera kukhala otani pa kugonana musanakwatirane?

Kodi Mulungu Amawaganiziradi Ana? 16

Kodi Mulungu adzachita chiyani kuti athetse kuzunzika kwa ana?

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

© Mikkel Ostergaard/Panos Pictures

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena