Zamkatimu
August 8, 2005
Kodi N’zotheka Kukhala Mopanda Mantha?
Anthu amaopa zinthu zambiri masiku ano. Kodi zidzatheka kukhala mopanda mantha tsiku lina?
4 N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Amakhala Mwamantha?
8 Kodi N’zotheka Kukhala Mopanda Mantha?
14 Kuyesera Kudyetsa Anthu Wani Biliyoni
18 Nkhani Yakale Inakhudza Mitima ya Anthu
19 Kodi Masoka Achilengedwe Akuwonjezeka?
21 Mmene Zochita za Anthu Zikuwonjezera Masoka Achilengedwe
26 Masoka Onse Adzatha Posachedwapa
28 Ndinakopeka ndi Mlengi Chifukwa cha Kukongola kwa Choonadi
32 Mmene Mungakhalire Bwenzi la Mulungu
Ndinakopeka ndi Mlengi Chifukwa cha Kukongola kwa Choonadi 28
Kodi zinatani kuti katswiri wa luso la ku Japan la kaikidwe ka maluwa afike pozindikira kuti kunja kuno kuyenera kukhala Mlengi?