Zamkatimu
September 8, 2004
Kodi Tsankho Lidzatha?
Tsankho limagawanitsa anthu ndipo lafika mpaka poyambitsa nkhondo. Kodi tsankho lingathetsedwe bwanji kuti lisadzakhaleponso mpaka kalekale?
3 Mitundu Yosiyanasiyana ya Tsankho
12 Achinyamata Amene Sachita Manyazi Kulankhula za Chikhulupiriro Chawo
14 Chinthu Chabwino Kuposa Kutchuka
19 Vuto la Mabanja Opanda Atate Likukula
21 Atate Amene Ana Amafunikira
24 Mmene Mungakhalire Tate Wabwino
31 “Mudzaŵerenga Liti Zonsezi?”
Kodi Ndingatani Kuti Ndipewe Kugonana Ndisanaloŵe M’banja? 28
Kugonana anthu asanaloŵe m’banja kwabweretsa mavuto aakulu. Kodi achinyamata angatani kuti apeŵe kugonana asanaloŵe m’banja n’kudziteteza ku mavuto?
[Chithunzi patsamba 2]
Kudera lapakati pa chigawo cha Tamil Nadu, ku India
Ana a fuko lodetsedwa ali kusukulu ya m’mudzi mwawo
[Mawu a Chithunzi]
© Mark Henley/Panos Pictures