Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g05 1/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2005
  • Nkhani Yofanana
  • Ulendo Wosaiwalika Wokaona Chigwa cha Ngorongoro
    Galamukani!—2005
  • Mulungu Akulonjeza Kuti Dzikoli Lidzakhalanso Bwino
    Galamukani!—2023
  • Kodi zinthu zofunika pa moyo wathu, monga chakudya, zidzatheratu padzikoli?
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Kodi Anthu Apitiriza Kuwononga Dzikoli N’kufika Poti Silingakonzedwenso?
    Nsanja ya Olonda—2014
Onani Zambiri
Galamukani!—2005
g05 1/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

January 8, 2005

Kodi Dziko Lathuli Lipulumuka?

Zinthu zachilengedwe za padziko pano zikutha modetsa nkhawa. Kodi ndani angathetse vutoli?

3 Dziko Lathuli Likusakazidwa Kwabasi

4 Zinthu Zachilengedwe Zikutha Padziko Pano

10 Dziko Lathuli Lidzapulumuka

15 Ulendo Wosaiwalika Wokaona Chigwa cha Ngorongoro

18 “Ndikanakonda Anthu Akanadziwa Zimenezi!”

19 Kunyanyira Kufuna Kukongola

20 Kuipa Kofunitsitsa Kukhala Wokongola

24 Kukongola Kofunika Kwambiri

26 Kwalembedwa Kuti Ndidzawaonanso

Kodi Ndingatani Mnyamata Amene Ndimamufuna Akandikana? 12

Kodi mtsikana angatani mnyamata amene amamufuna akamukana?

Kodi Kufatsa N’kupanda Mphamvu? 31

Anthu ambiri masiku ano angayankhe kuti inde n’kupanda mphamvu, koma Baibulo limasonyeza kuti si choncho ayi.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

COVER: NASA JSC

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena