Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 6/06 tsamba 27-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2006
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • FOTOKOZANI CHITHUNZICHI
  • ZINACHITIKA LITI?
  • NDINE NDANI?
  • NDINE NDANI?
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
Onani Zambiri
Galamukani!—2006
g 6/06 tsamba 27-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

FOTOKOZANI CHITHUNZICHI

1. Fanizo la Yesu pa Mateyu 13:3-9, 18-23, limati mbewu zinagwa pa malo anayi ati?

Lembani mzere wolumikiza yankho lanu lililonse ku chithunzichi.

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

2. Kodi mbewu ikuimira chiyani?

․․․․․

◼ Kambiranani: Kodi mungatani kuti muonetsetse kuti mtima wanu uli ngati dothi labwino? Kodi n’chifukwa chiyani kuchita zimenezo kuli kopindulitsa?

ZINACHITIKA LITI?

Lembani mzere wolumikiza chochitika chilichonse ku chaka chimene chinachitikira.

1943 B.C.E. 1919 1770 1728 1473 1066

3. Genesis 46:5-7

4. Genesis 12:4

5. Yoswa 2:1-21

NDINE NDANI?

6. Ndinkakhala ku Elikosi ndipo ndinanenera zinthu zoipira Nineve.

NDINE NDANI?

7. Dzina la mwamuna wanga wachiwiri linkatanthauza “Wokondedwa.” Dzina la mwamuna wanga woyamba linkatanthauza “Wopusa.”

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowekapo.

Tsamba 8 Kodi uchigawenga udzatha bwanji? (Mika 4:․․․)

Tsamba 9 Kodi mkwiyo wa munthu umalephera kuchita chiyani? (Yakobo 1:․․․)

Tsamba 10 Kodi ndalama zikhoza kuchita chiyani? (Mlaliki 7:․․․)

Tsamba 28 Kodi tchimo loyambirira linali chiyani? (Genesis 3:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali patsamba 27)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. M’mbali mwa njira, pamiyala, paminga, ndi pa nthaka yabwino.

2. Mawu a Ufumu.

3. 1728 B.C.E.

4. 1943 B.C.E.

5. 1473 B.C.E.

6. Nahumu.—Nahumu 1:1.

7. Abigayeli.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena