Kodi Mungayankhe Bwanji?
TCHULANI ANA AAMUNA 12 A YAKOBO
1. ․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․
․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․․

Lembani mzere kuchokera pa dzina la mwana wa Yakobo kufika pa mbadwa yake yodziwika kwambiri.
2. Yesu
3. Mose
4. Mfumu Sauli
◼ Kambiranani: N’chifukwa chiyani Yosefe ankadedwa ndi abale ake? Kodi mungatsanzire bwanji Yosefe ngati nthawi zina abale anu amakudani?
ZINACHITIKA LITI?
Tchulani amene analemba mabuku a m’Baibulo omwe ali m’munsimu, ndipo lembani mzere kuchokera pa bukulo kufika pa chaka chimene linamalizidwa kulembedwa.
607 B.C.E. 539 B.C.E. 40 C.E. 61-64 C.E. 65 C.E.
5. Maliro
6. 2 Timoteyo
7. Tito
NDINE NDANI?
8. Ine ndi mwana wanga wamkazi tinayamikiridwa ndi Paulo chifukwa chokhala ndi chikhulupiriro chopanda chinyengo.
NDINE NDANI?
9. Ndinapatsidwa mphamvu zoika akulu ku Kerete.
KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowapo.
Tsamba 6 Kodi chifukwa chimodzi chimene anthu amafera pa masoka achilengedwe n’chiti? (Mlaliki 9:․․․)
Tsamba 10 Kodi timadziwa bwanji kuti Yehova amaona moyo wa mwana kukhala wamtengo wapatali? (Salmo 139:․․․)
Tsamba 20 Kodi n’chifukwa chiyani Yehova amakukondani mosasamala za kumene mumachokera? (Machitidwe 10:․․․)
Tsamba 26 Kodi n’chifukwa chiyani kukhala osangalala kuli kofunika? (Miyambo 17:․․․)
Zithunzi Zoti Ana Apeze
Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pachithunzi chilichonse.
(Mayankho ali pa tsamba 22)
MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
1. Rubeni, Simeoni, Levi, Yuda, Zebuloni, Isakara, Dani, Gadi, Aseri, Nafitali, Yosefe, Benjamini.—Genesis 49:2-28.
2. Yuda.—Luka 3:33, 34.
3. Levi.—Eksodo 6:16, 18, 20.
4. Benjamini.—1 Samueli 9:1, 2, 15, 16.
5. Yeremiya, 607 B.C.E.
6. Paulo, 65 C.E.
7. Paulo, 61-64 C.E.
8. Loisi.—2 Timoteyo 1:5.
9. Tito—Tito 1:4, 5.