Kodi Mungayankhe Bwanji?
KODI PALI KUFANANA KOTANI?
1. Pa zochitika zomwe zalembedwa m’munsimu, lembani mzere kuzungulira zochitika zokhazo zomwe zinachitikira Mose ndi Yesu.
Anaitanidwa kuti achoke ku Igupto
Anapulumuka osaphedwa ali mwana
Anatulutsa madzi m’thanthwe
Anasala kudya masiku 40
Anaukitsa akufa
Anapachikidwa pa mtengo
Yehova anataya thupi lake
◆ Kodi Mose anaima liti pambali pa Yesu m’masomphenya?
․․․․․
◆ Kodi winanso ndani anaonekera naye limodzi?
․․․․․
◼ Kambiranani: Kodi Yesu anali mneneri ngati Mose m’njira zina ziti?—Machitidwe 3:22.
ZINACHITIKA LITI?
Lembani mzere kulumikiza chochitika chilichonse ndi chaka chomwe chinachitikira.
1077 B.C.E. Cha m’ma 940 Cha m’ma 844 Kuchokera mu 778 Kuchokera mu 322
2. Yesaya 1:1
3. Yona 1:14-17
NDINE NDANI?
5. Mwana wanga wamkazi anapha abale ake n’kulanda ufumu wa Yuda. Koma mofanana ndi ine, anali mfumukazi yomwe inafa mochita kuphedwa.
NDINE NDANI?
6. Ndinaneneratu malo amene Mesiya anadzabadwirako.
KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowapo.
Tsamba 11 N’chifukwa chiyani Mulungu amaona kuti magazi ndi opatulika? (Genesis 9:․․․)
Tsamba 13 Kodi bwato losodzera nsomba ku Galileya m’zaka 100 zoyambirira linkatha kunyamula anthu angati? (Yohane 21:․․․)
Tsamba 24 Kodi chimachitika n’chiyani tikaika zosowa za ena patsogolo pa zosowa zathu? (Miyambo 11:․․․)
Tsamba 29 Kodi tikudziwa bwanji kuti anthu akufa sakukhala kumwamba ngati angelo? (Mlaliki 9:․․․)
Zithunzi Zoti Ana Apeze
Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.
(Mayankho ali pa tsamba 27)
MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
1. Anaitanidwa kuti achoke ku Igupto. Anapulumuka osaphedwa ali mwana. Anasala kudya masiku 40. Yehova anataya thupi lake.
◆ M’masomphenya a kusandulika kwa Yesu.—Mateyu 17:1-3.
◆ Eliya.
2. Kuchokera mu 778 B.C.E.
3. Cha m’ma 844 B.C.E.
4. Cha m’ma 940 B.C.E.
5. Yezebeli.
6. Mika.—Mika 5:2.