Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 3/07 tsamba 19-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2007
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • KODI ZINACHITIKIRA KUTI?
  • ZINACHITIKA LITI?
  • NDINE NDANI?
  • NDINE NDANI?
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2007
g 3/07 tsamba 19-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

KODI ZINACHITIKIRA KUTI?

1. Kodi Mgonero wa Ambuye unachitikira kuti koyamba?

Lembani mzere mozungulira yankho lanu pa mapupa.

Nazarete

Yeriko

Yerusalemu

Betelehemu

◆ Kodi buledi wopanda chofufumitsa amaimira chiyani?

․․․․․

◆ Kodi vinyo wofiira amaimira chiyani?

․․․․․

◼ Kambiranani: Kodi Mgonero wa Ambuye umatikumbutsa chiyani? N’chiyani chimene chimakusangalatsani pa mwambo umenewu?

ZINACHITIKA LITI?

Tchulani anthu amene analemba mabuku a m’Baibulo amene ali m’munsiwa, ndipo lembani mzere wolumikiza buku ndi nthawi imene anamaliza kulilemba.

1077 B.C.E. 1040 B.C.E. 580 B.C.E 55 C.E 66 C.E

2. 2 Samueli

3. 2 Mafumu

4. 2 Akorinto

NDINE NDANI?

5. Anzanga anandibweretsera madzi kuti ndimwe, koma ndinawathira pansi ngati magazi.

NDINE NDANI?

6. Ena anati iwowo ndi anthu anga; ena anati iwowo ndi anthu a Paulo, a Apolo, kapena a Khristu.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo tchulani mavesi a m’Baibulo omwe akusowa.

Tsamba 8 Kodi timafunikira kutsimikizira chiyani? (Afilipi 1:․․․)

Tsamba 9 Kodi mungakhale bwanji anzeru? (Miyambo 13:․․․)

Tsamba 20 Kodi ndani amene adzakhale wamkulu mu “ufumu wa kumwamba”? (Mateyo 18:․․․)

Tsamba 29 Kodi ndi ndani amene sadzalowa mu Ufumuwo? (Aefeso 5:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani nokha zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali patsamba 19)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1.Yerusalemu—Mateyo 21:10, 17, 18; 26:17-19.

◆ Thupi la Yesu.—Mateyo 26:26.

◆ Magazi a Yesu.—Mateyo 26:27, 28.

2. Gadi, Natani, 1040 B.C.E

3. Yeremiya, 580 B.C.E.

4. Paulo, 55 C.E.

5. Davide.—2 Samueli 23:15-17.

6. Kefa, kapena Petulo.—Yohane 1:42; 1 Akorinto 1:12.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena