Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 8/07 tsamba 27-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2007
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • KODI ZINACHITIKIRA KUTI?
  • ZINACHITIKA LITI?
  • NDINE NDANI?
  • NDINE NDANI?
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2007
g 8/07 tsamba 27-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

KODI ZINACHITIKIRA KUTI?

1. Kodi izi ziyenera kuti zinachitikira pafupi ndi mzinda uti?

Lembani mzere mozungulira yankho lanu pa mapupa.

Babulo

Susani

Uri

◆ Tchulani mayina achiheberi a Aisiraeli atatuwa.

․․․․․

․․․․․

․․․․․

◆ N’chifukwa chiyani iwo sakugwada ngati anzawo ena onse?

․․․․․

◼ Kambiranani: Kodi anthu ena angakuuzeni kulambira mafano otani? Kodi mungatsatire bwanji chitsanzo cha Aheberi atatuwa?

ZINACHITIKA LITI?

Tchulani anthu amene analemba mabuku a m’Baibulo amene ali m’munsiwa, ndipo lembani mzere wolumikiza buku ndi nthawi imene anamaliza kulilemba.

1000 B.C.E. 607 B.C.E. 36 C.E. 51 C.E. 61-64 C.E.

2. 1 Timoteyo

3. Mlaliki

4. 2 Atesalonika

NDINE NDANI?

5. Mayi anga anandilangiza ndi uthenga wofunika.

NDINE NDANI?

6. Dzina langa m’Chigiriki ndi Sila, ndipo zikuoneka kuti Petulo, Paulo, ndi Luka ananditchulanso m’mabuku awo.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo tchulani mavesi a m’Baibulo omwe akusowa.

Tsamba 4 Kodi chikondi n’chiyani? (Akolose 3:․․․)

Tsamba 6 Kodi makolo amene amakonda ana awo amachita chiyani? (Miyambo 13:․․․)

Tsamba 11 Kodi Mfumu Davide inakondwera liti? (Salmo 122:․․․)

Tsamba 14 Kuti tipewe miseche, kodi tiyenera kuyesetsa kuchita chiyani? (1 Atesalonika 4:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani nokha zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali pa tsamba 27)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Babulo.—Danieli 3:1.

◆ Hananiya, Misaeli, ndi Azariya.—Danieli 1:7.

◆ Ankalambira Yehova yekha.—Danieli 3:16-18.

2. Paulo, 61-64 C.E.

3. Solomo, isanakwane 1000 B.C.E.

4. Paulo, 51 C.E.

5. Lemueli.—Miyambo 31:1.

6. Silivano.—1 Atesalonika 1:1.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena