Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 1/07 tsamba 26-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2007
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • FOTOKOZANI FANIZO
  • ZINACHITIKA LITI?
  • NDINE NDANI?
  • NDINE NDANI?
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2007
g 1/07 tsamba 26-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

FOTOKOZANI FANIZO

1. M’fanizo la Yesu lolembedwa pa Mateyo 18:23-35, kodi kapolo ankafuna kuti mfumu imuchitire chiyani?

․․․․․

2. Kodi kapolo woyambirirayo anachita chiyani kwa kapolo m’nzake?

․․․․․

3. N’chifukwa chiyani mfumu inakwiya ndi kapolo woyamba uja?

․․․․․

◼ Kambiranani: Kodi mwakhululukirapo liti munthu wina? Kodi munthu ameneyo anakulakwirani chiyani? N’chifukwa chiyani munam’khululukira?

ZINACHITIKA LITI?

Tchulani munthu kapena anthu amene analemba mabuku a m’Baibulo amene ali m’munsiwa, ndipo lembani mzere kuchokera padzina la bukulo kufika pachaka chimene bukulo linamalizidwa kulembedwa.

1657 B.C.E.

1513 B.C.E. Cha m’ma 1100 B.C.E. Cha m’ma 56 C.E. Cha m’ma 61 C.E.

4. Genesis

5. Oweruza

6. Machitidwe

NDINE NDANI?

7. Ana anga amapasa anakhala makolo a mitundu iwiri ikuluikulu.

NDINE NDANI?

8. Mayere sanandigwere kuti ndikhale mtumwi.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani mavesi kapena vesi la m’Baibulo lomwe likusowapo.

Tsamba 3 Kodi ndi mavuto ati okhudza thanzi amene adzathetsedwe posachedwapa? (Yesaya 35:․․․)

Tsamba 11 N’chiyani chingakupangitseni kukhulupirira kuti matenda adzatha? (Luka 18:․․․)

Tsamba 20 Kodi chingalawa cha Nowa chinali chotalika bwanji m’mbali zake zosiyanasiyana? (Genesis 6:․․․)

Tsamba 30 Kodi muyenera kupewa khalidwe lotani ndipo ndi maganizo otani amene muyenera kukhala nawo musanaganize zolowa m’banja? (Aefeso 4:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pachithunzi chilichonse.

(Mayankho ali patsamba 26)

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Am’chitire chifundo pangongole yake.

2. Anam’ponya m’ndende.

3. Chifukwa kapoloyu sanasonyeze chifundo.

4. Mose, mu 1513 B.C.E.

5. Samueli, cha m’ma 1100 B.C.E.

6. Luka, cha m’ma 61 C.E.

7. Rabeka.—Genesis 25:21-23.

8. Barasaba.—Machitidwe 1:23-26.

[Mawu a Chithunzi patsamba 31]

Middle circle: Scott Bauer/Agricultural Research Service, USDA

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena