Zamkatimu
March 2008
Kodi Pali Chipembedzo Choona Chimodzi Chokha?
Nthawi zambiri anthu amati choonadi chimapezeka m’zipembedzo zonse. Koma kodi zipembedzo zonse n’zovomerezeka kwa Mulungu? Kodi n’zotheka kuti choonadi chimapezeka m’zipembedzo zosiyanasiyana? Kodi Yesu anaphunzitsa chiyani pankhaniyi?
3 Kodi Pali Chipembedzo Choona Chimodzi Chokha?
5 Ndani Angatisonyeze Chipembedzo Choona?
7 Kodi Mungapeze Bwanji Chipembedzo Choona?
12 Kulalikira Uthenga Wabwino M’madera Akutali
16 N’chifukwa Chiyani Chimatchedwa Chilumba Chachikulu?
18 Anyani Odabwitsa a M’matanthwe
22 Miyambo Yakale Ilipobe ku Mexico
28 “Tsiku Limene Kunada Masana”
32 Imfa Yofunika Koposa M’mbiri Yonse ya Anthu
Kodi Zikhulupiriro za Makolo N’zogwirizana ndi Baibulo? 10
Kodi Akhristu a m’nthawi ya atumwi ankaona bwanji zikhulupiriro za makolo? Kodi munthu angasiye bwanji zikhulupiriro zimenezi?
Kodi Kutukwana N’kulakwadi? 19
Kodi kutukwana kumasonyeza chiyani za munthu wotukwanayo? Kodi kutukwana kuli ndi vuto lanji? Nanga mungakupewe bwanji?