Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 4/08 tsamba 1-3
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2008
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Oona za Ndege Amakutetezani Bwanji? 13
  • Kuyenda pa Boti ku Kerala
    Galamukani!—2008
  • Mapazi a Nalimata
    Galamukani!—2008
  • Oona za Ndege Amakutetezani Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Mmene Mungachitire ndi Mavuto a Kuchuluka kwa Magalimoto Pamsewu
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 4/08 tsamba 1-3

Zamkatimu

April 2008

Kodi Tili M’masiku Otsiriza?

Kodi mawu a m’Baibulo akuti “masiku otsiriza” amatanthauza chiyani? Kodi mawuwa amam’khudza bwanji munthu aliyense? Kodi zinthu zidzakhala bwino m’tsogolo?

3 Kodi Ndi Masiku Otsiriza a Chiyani?

4 Kodi Masiku Otsiriza Ndi Ati?

8 Masiku Otsiriza Akadzatha Zinthu Zidzakhala Bwanji?

10 Phunzirani Kuimba Mwaluso

16 Mafuta a Golide a ku Mediterranean

20 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Mulungu Amafuna Kuti Muzichita Chiyani?

22 Kuyenda pa Boti ku Kerala

26 Mapazi a Nalimata

Analengedwa Mwaluso

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Mmene Achinyamata Angathetsere Kuvutika Maganizo

Oona za Ndege Amakutetezani Bwanji? 13

Nthawi iliyonse ndege zambirimbiri zimakhala zikuuluka, ndiye kodi oona za kayendedwe ka ndege amathandiza bwanji kuti ndegezi zisagundane? Kodi mumakhaladi otetezeka mukakwera ndege?

N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Sandikhulupirira? 27

Kodi achinyamata angachite chiyani kuti makolo awo aziwakhulupirira ndi kuwalemekeza?

[Mawu a Chithunzi patsamba 3]

© Jacob Silberberg/​Panos Pictures

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena