Zamkatimu
September 2008
Kodi Amene Ali Kumanda Adzakhalanso ndi Moyo?
Onani umboni wakuti amene ali kumanda adzakhalanso ndi moyo. Onaninso mmene zimenezi zidzathekere ndiponso zomwe Baibulo limanena za mmene moyo udzakhalire.
3 Kodi Imfa Ndi Mapeto a Zonse?
4 N’zotheka Ndithu Kuti Amene Ali Kumanda Adzakhalenso ndi Moyo
11 Galamukani! Inamuthandiza Mosayembekezera
12 Mulungu Anandithandiza Kugonjetsa Mayesero
22 Kulimbana ndi Matenda a Asperger
32 “Sindinkadziwa Kuti Mulungu Ali ndi Dzina”
Maloboti, omwe anthu amati ndi makina anzeru, amathandiza kwambiri m’mafakitale ambiri. Kodi adzakhudza bwanji tsogolo lanu?
Kodi Ndingatani ndi Vuto la Kupanikizika Kusukulu? 26
Dziwani zifukwa zikuluzikulu zimene zimachititsa achinyamata kupanikizika kusukulu ndiponso zinthu zimene zingawathandize kuchepetsa kupanikizikako.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
NASA/JPL/Cornell University