Zamkatimu
November 2008
Kodi Mungatani Kuti Zinthu Zizikuyenderani?
Anthu ambiri amati munthu amene zikumuyendera bwino ndi amene ali wotchuka, wolemera kapena wamphamvu. Koma kodi zimenezi n’zimene zimasonyezadi kuti munthu zikumuyendera? Werengani kuti mudziwe zenizeni za nkhani imeneyi ndi kuona kuti munthu aliyense zinthu zikhoza kumamuyendera bwino.
3 Ngati Zinthu Sizikuyenda Bwino
4 Kodi Ndani Angatithandize Kuti Zinthu Zizitiyendera Bwino?
6 Mfundo 6 Zokuthandizani Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino
11 Kuunika M’thupi—M’malo Mopanga Opaleshoni
15 ‘Kulowa pa Diso la Singano’
29 Anthu a ku Okinawa Amakhala ndi Moyo Zaka Zambiri—Kodi Chinsinsi Chawo N’chiyani?
32 Mmene Mungakhalire Bwenzi la Mulungu
Kodi Maganizo a Mulungu Ndi Otani pa Zinthu Zothandiza Popemphera? 18
Anthu ambiri amene amati ndi Akhristu komanso amene si Akhristu amapemphera pogwiritsa ntchito zinthu zothandiza popemphera komanso pochita miyambo inayake yachipembedzo. Kodi maganizo a Mulungu ndi otani pankhani imeneyi?
N’chifukwa Chiyani Nsomba Zikusowa? 20
Kupha nsomba mosakaza kukupangitsa anthu kuda nkhawa kuti adzasowa chakudya m’tsogolo. Werengani kuti muone mmene vutoli linayambira ndiponso ngati zinthu zingasinthe.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
© Janis Miglavs/DanitaDelimont.com