Zamkatimu
June 2009
Kodi Kuchotsa Mimba N’koipa Chifukwa Chiyani?
Kodi moyo wa munthu umayamba liti? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Baibulo limanena zomwe zikugwirizananso ndi sayansi.
3 Kuchotsa Mimba Si Njira Yabwino
5 Kodi Moyo wa Munthu Umayamba Liti?
6 Chifukwa Chake Sitinachotse Mimba
10 Kodi Pali Vuto Lililonse ndi Kukhalitsa Padzuwa?
12 Ndinamasulira Mabuku Mobisa kwa Zaka 30
16 Mzinda wa Plovdiv Ndi Wakale Kwambiri
28 Thandizani Ana Anu Kuti Akule Bwino
30 Wodwala Ali Ndi Ufulu Wosankha
32 Msonkhano Wachigawo wa Mboni za Yehova Wakuti: “Khalani Maso”
Kodi Muyenera Kuopa Anthu Akufa? 22
N’chifukwa chiyani anthu ambiri m’mayiko osiyanasiyana amaopa anthu akufa? Kodi n’chiyani chingathandize anthu kuthetsa mantha amenewa?
Achinyamata a Katolika Anauzidwa Kuti Azilalikira 24
Mwambo wa Tsiku la Achinyamata Padziko Lonse wa 2008, unachitikira ku Australia ndipo kunali anthu ambiri zedi. Anthu enanso okwana 500 miliyoni anaonera mwambowu pa TV. Kodi mwambowu unasonyeza chiyani za chikhulupiriro cha achinyamata?