Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 9/09 tsamba 29-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2009
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Pachithunzichi Pakusowa Chiyani?
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Kodi Mukudziwa Zotani Zokhudza Woweruza Baraki?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Zoti Banja Likambirane
    Galamukani!—2010
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
Onani Zambiri
Galamukani!—2009
g 9/09 tsamba 29-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Pachithunzichi Pakusowa Chiyani?

Werengani Machitidwe 5:1-5. Ndiyeno yang’anani pachithunzipa. Kodi ndi zinthu zotani zimene zikusowapo? Lembani mayankho anu m’mizere ili m’munsiyi, ndipo malizitsani kujambula chithunzichi poika zinthu zimene zikusowapo.

1. ․․․․․

2. ․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi mukuganiza kuti Hananiya ananama chifukwa chiyani? Kodi tikuphunzira chiyani pankhani imeneyi?

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunso awa ndipo tchulani mavesi a m’Baibulo omwe akusowa.

TSAMBA 11 Kodi anthu ochimwa akafa amapita kuti? Genesis 3:․․․

TSAMBA 11 Kodi akufa amadziwa kanthu kalikonse? Mlaliki 9:․․․

TSAMBA 17 Kodi tonsefe timatani pa zinthu zambiri? Yakobe 3:․․․

TSAMBA 17 Kodi ndi zinthu ziti zomwe ziyenera kuchotsedwa mwa ife? Aefeso 4:․․․

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pachithunzi chilichonse.

Kodi Mukudziwa Zotani Zokhudza Woweruza Baraki?

Werengani Oweruza 4:1-24. Ndiyeno yankhani mafunso otsatirawa.

3. ․․․․․

Tchulani mneneri wamkazi yemwe anathandiza Baraki?

4. ․․․․․

Kodi Baraki anapulumutsa Aisiraeli kwa mfumu iti ya ku Kanani?

5. ․․․․․

Kodi ndi zoona kapena zonama? Woweruza Baraki anakhala ndi moyo Yoswa atamwalira kale.

KAMBIRANANI:

Kodi akazi anathandiza bwanji kuti Aisiraeli agonjetse Akanani? Kodi akazi masiku ano akugwira ntchito yofunika yotani potumikira Mulungu?

◼ Mayankho ali patsamba  29

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Hananiya alibe ndalama.

2. Mtumwi Petulo palibe pachithunzichi.

3. Debora.—Oweruza 4:4-9.

4. Yabini.—Oweruza 4:2.

5. Zoona.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena